Nkhani zakubedwa kwa ndalama m’boma ya kachigeti tsopano yayamba koneka mutu wake. Padakali ano, anthu atatu apezeka olakwa pamlandu owaganizira kuti akukhudzidwa ndi kusolola kwa ndalama za boma. M’sabatayi, bwalo la milandu la majisitireti ku Lilongwe lidagamula Victor Sithole kuti akaseweze kundende zaka 9 atamupeza wolakwa pamlandu wopezeka ndi ndalama zakunja popanda chilolezo, kupezeka ndi [&hellip
The post Milandu ya ‘kashigeti’ yayamba kusongola appeared first on The Nation Online.