Nthumbwana za ng’ombe kapena mbuzi zimaperekedwa kwa akuluakulu monga mafumu kapena alendo pakakhala zochitika. Ambirinso amakonda kudya nthumbwana ngati ndiwo pomwe ena amangokhwasula. Komatu pali chiwalo china panthumbwana chimene ena amakhulupirira kuti nchoyenera kudya abusa kapena kuti osamalira ziweto. Nidacheza ndi Vincent Kalimba yemwe akulongosola motere: Kodi zolemba munthu ntchito yoweta ziweto kwanu zimachitika? Kwabasi [&hellip
The post Kucheza: Chidya abusa–Nthumbwana zodya olisha ziweto okha appeared first on The Nation Online.