Ndani afika m’khonde. Mphunzitsi wa timu ya Flames Under 20, Ernest Mtawali, wati mtima wake uli podzagwetsa timu yachisodzera ya DR Congo yomwe masewero ake ali pa Kamuzu Stadium pa 10 May. Masewerowa akudza pamene Malawi idakwanitsa kudutsa m’ndime yoyamba ya masewero a CAF pogwetsa Botswana usiku wa Lachisanu lapita m’dziko lawo. Malawi idapuntha Botswana [&hellip
The post U-20 yakonzeka kupha DR Congo appeared first on The Nation Online.