Quantcast
Channel: Nation Online
Viewing all articles
Browse latest Browse all 43007

‘Kubazira’ woyamba mabere

$
0
0

Zikhulupiriro ndi miyambo ina koma kuondetsa. Ku Nsanje akuti mtsikana akangotukwana akulu (akangomera mabere) ‘amamubazira’ kuti asakumane ndi zokhoma mpaka atakalowa m’banja akadzavinidwa.Pochita mwambowu ati muyenera muphike kansima, ndiwo zake nyemba ndipo patsikulo makolo m’nyumbamo agonane nthawiyi isadakwane.Zimatani?BOBBY KABANGO akucheza ndi Harry Ngalu. Tidziwane wawa… Ndine mfumu ya Chitonga, ndine nyakwawa ndipo ndimadziwika ndi dzina [&hellip

The post ‘Kubazira’ woyamba mabere appeared first on The Nation Online.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 43007

Trending Articles