Tiwonge Hango ndi mnyamata wofatsa, koma akagwira chimkwezamawu pansanja ndi kuyamba kuimba, simungamudziwe kuti ndi yemwe uja—mawu ake amakhala ngati a mnjelo. Chifukwa cha mawu ake anthetemya Tiwonge wakhala akupambanapo mphotho zosiyanasiyana. Kodi iyeyu ndani ndipo adayamba bwanji kuimba? Dailes Banda adacheza naye motere: Uli bwanji Tiwonge? Ine ndili bwino, kaya iweyo? Shapu! Tandiuze, [&hellip
The post Tiwonge Hango: Amagomera Wambali appeared first on The Nation Online.