Alimi a fodya ali ndi chiyembekezo choti apha makwacha ochuluka chaka chino ngati mitengo yomwe ogula mbewu akupereka kuokushoni ingapitirire kapena kukwera kuposa apa. Potsegulira malondawa Lolemba lapitali kumsika wa fodya ku Lilongwe Auction Floors, fodya wodula kwambiri amamugula pamtengo wa $2.05 (K877.40) pa kilogalamu ndipo wotsika kwambiri adali pa $1 (K428). Mmodzi mwa alimi [&hellip
The post Msiska wa fodya wayamba bwino appeared first on The Nation Online.