Mkulu wa nthambi yoyendetsa ntchito za ulangizi mu Unduna wa Malimidwe Stella Kamkwamba wati alimi ochenjera amakhala ndi ndondomeko ya mmene agwirire ntchito yawo kuti asasokonezeke ndi mavuto odza mwadzidzidzi. Kamkwamba wati mlimi yemwe amadziwiratu ntchito yomwe akuyenera kugwira nthawi zonse amakwanitsa kuthana ndi mavuto monga a tizilombo, matenda ndi nyengo chifukwa ntchito yake siikhala [&hellip
The post Ndondomeko Omathandiza appeared first on The Nation Online.