Quantcast
Channel: Nation Online
Viewing all articles
Browse latest Browse all 43640

Adzukulu okwiya akumba manda panyumba ya mfumu

$
0
0

Nyakwawa Makolera kuloza nyumba ya mfumu idagumulidwayoAdzukulu a m’mudzi mwa Gulupu Layton Yesaya kwa T/A Chanthunya ku Balaka masiku apitawa adakumba manda pakhomo pa mfumu ya m’mudzimo ati chifukwa chokwiya mfumuyo itakana kutsekula khomo la kumanda. Malinga ndi Jonasi Mlauzi wa m’mudzimo, chidatsitsa dzaye kuti njovu ithyoke mnyanga n’choti bambo wina wa m’mudzi mwa Mbewe atamwalira pa 13 August uthenga wa [&hellip

The post Adzukulu okwiya akumba manda panyumba ya mfumu appeared first on The Nation Online.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 43640